9 Ndipo padzakhala tsiku lomwelo, ati Yehova, kuti mtima wa mfumu udzatayika, ndi mitima ya akuru; ndipo ansembe adzazizwa, ndi aneneri adzadabwa.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4
Onani Yeremiya 4:9 nkhani