10 Ndipo ndinati, Ha, Yehova Mulungu! ndithu mwanyenga kwambiri anthu awa ndi Yerusalemu, ndi kuti, Mu'dzalandira mtendere; koma lupanga lafikira pamoyo.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4
Onani Yeremiya 4:10 nkhani