Yeremiya 4:11 BL92

11 Pa nthawi yomweyo adzati kwa anthu awa ndi kwa Yerusalemu, Mphepo yotentha yocokera ku mapiri oti se m'cipululu yopita kwa mwana wamkazi wa anthu anga, yosaungula, yosayeretsa;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4

Onani Yeremiya 4:11 nkhani