8 Ndipo wakufunkha adzafikira pa midzi yonse, sudzapulumuka mudzi uli wonse; cigwa comwe cidzasakazidwa, ndipo cidikha cidzaonongedwa; monga wanena Yehova.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48
Onani Yeremiya 48:8 nkhani