Yeremiya 5:4 BL92

4 Ndipo ine ndinati, Ndithu amenewo ali aumphawi; ali opusa; pakuti sadziwa njira ya Yehova, kapena ciweruzo ca Mulungu wao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 5

Onani Yeremiya 5:4 nkhani