Yeremiya 50:16 BL92

16 Muwathe ofesa ku Babulo, ndi iwo amene agwira zenga nyengo ya masika; cifukwa ca lupanga losautsa adzatembenukira yense kwa anthu ace, nadzathawira yense ku dziko lace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:16 nkhani