17 Israyeli ndiye nkhosa yolowerera, mikango yampitikitsa, poyamba inamudya mfumu ya Asuri; ndipo pomariza Nebukadirezara uyo watyola mafupa ace.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50
Onani Yeremiya 50:17 nkhani