Yeremiya 50:18 BL92

18 Cifukwa cace atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Taonani, ndidzalanga mfumu ya ku Babulo ndi dziko lace, monga ndinalanga mfumu ya Asuri.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:18 nkhani