Yeremiya 50:24 BL92

24 Ndakuchera iwe msampha, ndi iwenso wagwidwa, iwe Babulo, ndipo sunadziwa, wapezeka, ndiponso wagwidwa, cifukwa walimbana ndi Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:24 nkhani