Yeremiya 50:25 BL92

25 Yehova watsegula pa nyumba ya zida zace, ndipo waturutsa zida za mkwiyo wace; pakuti Ambuye Yehova wa makamu, ali ndi nchito m'dziko la Akasidi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:25 nkhani