31 Taonani, nditsutsana nawe, wonyada iwe, ati Ambuye, Yehova wa makamu; pakuti tsiku lako lafika, nthawi imene ndidzakulanga iwe.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50
Onani Yeremiya 50:31 nkhani