32 Ndipo wonyadayo adzakhumudwa nadzagwa, ndipo palibe amene adzamuutsa iye; ndipo Ine ndidzayatsa moto m'midzi yace, ndipo udzatentha onse akumzungulira iye.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50
Onani Yeremiya 50:32 nkhani