33 Yehova wa makamu atero: Ana a Israyeli ndi ana a Yuda asautsidwa pamodzi; ndipo onse amene anawagwira ndende awagwiritsitsa; akana kuwamasula.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50
Onani Yeremiya 50:33 nkhani