34 Mombolo wao ngwa mphamvu; dzina lace Yehova wa makamu: adzawanenera mlandu wao ndithu; kuti apumitse dziko lapansi, nadzidzimutse okhala m'Babulo.
Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50
Onani Yeremiya 50:34 nkhani