Yeremiya 50:5 BL92

5 Adzafunsira Ziyoni nkhope zao zirikuyang'ana kumeneko, ndi kuti, Tiyeni inu, dzilumikizeni kwa Yehova m'cipangano ca muyaya cimene sicidzaiwalika.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:5 nkhani