Yeremiya 50:6 BL92

6 Anthu anga anakhala nkhosa zotayika; abusa ao anazisokeretsa pa mapiri onyenga; acoka kuphiri kunka kucitunda; aiwala malo ao akupuma.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:6 nkhani