Yeremiya 7:28 BL92

28 Ndipo udzati kwa iwo, Umene ndi mtundu wosamvera mau a Yehova Mulungu wao, wosalola kulangizidwa, coonadi catha, cadulidwa pakamwa pao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 7

Onani Yeremiya 7:28 nkhani