Yeremiya 7:33 BL92

33 Ndipo mitembo ya anthu awa idzakhala zakudya za mbalame za mlengalenga, ndi za zirombo za dziko lapansi; palibe amene adzaziopsa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 7

Onani Yeremiya 7:33 nkhani