Yeremiya 7:34 BL92

34 Ndipo ndidzaletsa m'midzi ya Yuda, ndi m'miseu ya Yerusalemu, mau akukondwa ndi mau akusekera, ndi mau a mkwati ndi mau a mkwatibwi; pakuti dziko lidzasanduka bwinja.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 7

Onani Yeremiya 7:34 nkhani