Yeremiya 25:31 BL92

31 Phokoso lidzadza ku malekezero a dziko lapansi; pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi mitundu ya anthu, adzatsutsana ndi anthu onse; koma oipa, adzawapereka kulupanga, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25

Onani Yeremiya 25:31 nkhani