Yeremiya 25:32 BL92

32 Yehova wa makamu atero, Taonani, zoipa zidzaturuka ku mtundu kunka m'mitundu, ndipo namondwe adzauka kucokera ku malekezero a dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25

Onani Yeremiya 25:32 nkhani