Yeremiya 50:12 BL92

12 amai anu adzakhala ndi manyazi ambiri; amene anakubalani adzathedwa nzeru; taonani, adzakhala wapambuyo wa amitundu, cipululu, dziko louma, bwinja.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:12 nkhani