Yeremiya 50:13 BL92

13 Cifukwa ca mkwiyo wa Yehova sadzakhalamo anthu, koma padzakhala bwinja; onse akupita pa Babulo adzadabwa, adzatsonyera pa zobvuta zace zonse.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:13 nkhani