Yeremiya 50:14 BL92

14 Gubani ndi kuzungulira Babulo kumenyana naye, inu nonse okoka uta; mumponyere iye, osaderera mibvi; pakuti wacimwira Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:14 nkhani