Yesaya 1:10 BL92

10 Imvani mau a Yehova inu olamulira a Sodomu, cherani makutu ku cilamulo ca Mulungu wathu, inu anthu a Gomora.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 1

Onani Yesaya 1:10 nkhani