Yesaya 1:20 BL92

20 koma ngati mukana ndi kupanduka, mudzathedwa ndi lupanga; cifukwa m'kamwa mwa Yehova mwatero.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 1

Onani Yesaya 1:20 nkhani