Yesaya 1:23 BL92

23 Akuru ako apanduka, ali anzao a mbala; onse akonda mitulo, natsata zokometsera mirandu; iwo saweruzira amasiye; ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye suwafika.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 1

Onani Yesaya 1:23 nkhani