26 ndidzabweza oweruza ako monga poyamba, ndi aphungu ako monga paciyambi; pambuyo pace udzachedwa Mudzi wolungama, mudzi wokhulupirika.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 1
Onani Yesaya 1:26 nkhani