Yesaya 1:29 BL92

29 Cifukwa adzakhala ndi manyazi, cifukwa ca mitengo yathundu munaikhumba, ndipo inu mudzagwa nkhope, cifukwa ca minda imene mwaisankha.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 1

Onani Yesaya 1:29 nkhani