31 Ndimo wamphamvu adzakhala ngati cingwe cabwazi, ndi nchito yace ngati nthethe; ndipo zonse zidzayaka moto pamodzi, opanda wozimitsa.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 1
Onani Yesaya 1:31 nkhani