Yesaya 10:7 BL92

7 Koma iye safuna cotero, ndipo mtima wace suganizira cotero, koma mtima wace ulikufuna kusakaza, ndi kuduladula amitundu osawerengeka.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 10

Onani Yesaya 10:7 nkhani