Yesaya 11:10 BL92

10 Ndipo padzakhala tsiku lomwelo, kuti muzu wa Jese umene uima ngati mbendera ya mitundu ya anthu, amitundu adzafunafuna uwu; ndipo popuma pace padzakhala ulemerero.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 11

Onani Yesaya 11:10 nkhani