Yesaya 12:2 BL92

2 Taonani, Mulungu ndiye cipulumutso canga; ndidzakhulupira, sindidzaopa; pakuti Yehova Mwini ndiye mphamvu yanga ndi nyimbo yanga, Iye ndiye cipulumutso canga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 12

Onani Yesaya 12:2 nkhani