4 Tsiku lomwelo mudzati, Muyamikire Yehova, bukitsani dzina lace, mulalikire macitidwe ace mwa mitundu ya anthu, munene kuti dzina lace lakwezedwa.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 12
Onani Yesaya 12:4 nkhani