14 Ndipo padzakhala kuti monga mbawala yothamangitsidwa, ndi monga nkhosa zosazisonkhanitsa anthu, adzatembenukira yense kwa anthu ace, nathawira yense ku dziko lace.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 13
Onani Yesaya 13:14 nkhani