Yesaya 13:4 BL92

4 Mau a khamu m'mapiri, akunga amtundu waukuru wa anthu, mau a phokoso la maufumu a mitundu yosonkhanidwa! Yehova wa makamu asonkhanitsa khamu kunkhondo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 13

Onani Yesaya 13:4 nkhani