8 ndipo adzaopa; zowawa ndi masauko zidzawagwira; ndipo adzamva zowawa, ngati mkazi wakubala; adzazizwa wina ndi wina; nkhope zao zidzanga malawi a moto.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 13
Onani Yesaya 13:8 nkhani