Yesaya 14:3 BL92

3 Ndipo padzakhala tsiku loti Yehova adzakupumitsa cisoni cako, ndi nsautso yako, ndi nchito yako yobvuta, imene anakugwiritsa,

Werengani mutu wathunthu Yesaya 14

Onani Yesaya 14:3 nkhani