8 Inde, milombwa ikondwera ndi iwe, ndi mikungudza ya Lebano, ndi kunena, Cigwetsere iwe pansi, palibe wokwera kudzatidula ife.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 14
Onani Yesaya 14:8 nkhani