12 Ndipo padzakhala kuti pamene Moabu adzadzionetsa yekha, ndi kudzitopetsa pamsanje, ndipo kufika ku malo ace oyera kudzapemphera, sadzapindulapo kanthu.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 16
Onani Yesaya 16:12 nkhani