4 Opitikitsidwa a Moabu akhale ndi iwe, khala iwe comphimba pamaso pa wofunkha; pakuti kumpambapamba kwalekeka, kufunkha kwatha, opondereza atsirizika m'dziko.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 16
Onani Yesaya 16:4 nkhani