6 Ife tinamva kunyada kwa Moabu, kuti iye ali wonyada ndithu; ngakhale kudzitama kwace, ndi kunyada kwace ndi mkwiyo wace; matukutuku ace ali acabe.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 16
Onani Yesaya 16:6 nkhani