14 Pa nthawi ya madzulo, taonani kuopsya; kusanace, iwo palibe. Ili ndi gawo la iwo amene atifunkha ndi ici ciwagwera omwe alanda zathu.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 17
Onani Yesaya 17:14 nkhani