6 Adzasiyira mbalame zakulusa za m'mapiri ndi zirombo za dziko nthambizo, ndipo mbalame zakulusa zidzakhalapo m'dzinja, ndi zirombo zonse za dziko zidzakhalapo m'malimwe.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 18
Onani Yesaya 18:6 nkhani