Yesaya 19:11 BL92

11 Akalonga a Zoani apusa ndithu; uphungu wa aphungu anzeru a Farao wasanduka wopulukira; bwanji iwe unena kwa Farao, Ine ndine mwana wa anzeru, mwana wa mafumu akale?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 19

Onani Yesaya 19:11 nkhani