Yesaya 19:25 BL92

25 pakuti Yehova wa makamu wadalitsa iwo, ndi kuti, Odalitsika Aigupto anthu anga, ndi Asuri nchito ya manja anga, ndi Israyeli colowa canga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 19

Onani Yesaya 19:25 nkhani