Yesaya 2:19 BL92

19 Anthu adzalowa m'mapanga a m'matanthwe, ndi m'maenje apansi, kuthawa kuopsya kwa Yehova, ndi ulemerero wacifumu wace, podzuka Iye kugwedeza dziko ndi mphamvu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 2

Onani Yesaya 2:19 nkhani