Yesaya 21:16 BL92

16 Pakuti Ambuye ana tero kwa ine, Cisanapite caka malinga ndi zaka za wolembedwa nchito ulemerero wonse wa Kedara udzagoma;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 21

Onani Yesaya 21:16 nkhani