Yesaya 22:13 BL92

13 koma taonani, kukondwa, ndi kusekerera, ndi kupha ng'ombe, ndi kupha nkhosa, ndi kudya nyama, ndi kumwa vinyo; tiyeni tidye ndi kumwa, cifukwa mawa tidzafa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 22

Onani Yesaya 22:13 nkhani