Yesaya 23:16 BL92

16 Tenga mngoli, yendayenda m'mudzi, iwe mkazi wadama, amene unaiwalika; yimba zokoma, curukitsa nyimbo, kuti ukumbukiridwe.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 23

Onani Yesaya 23:16 nkhani